CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Yehova Anamenyera Nkhondo Aisiraeli
Mafumu 5 anagwirizana zomenyana ndi Agibeoni komanso Aisiraeli (Yos 10:5; it-1 50)
Yehova anamenyana ndi mafumuwo (Yos 10:10, 11; it-1 1020)
Yehova anachititsa kuti dzuwa liime (Yos 10:12-14; w04 12/1 11 ¶1)
Tikamazunzidwa timakhulupirira kuti Yehova atithandiza kukhalabe okhulupirika. Timadziwa kuti ndi thandizo lake, palibe boma lililonse limene lingatilepheretse kumulambira.