October 18-24
YOSWA 12-14
Nyimbo Na. 69 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Muzitumikira Yehova Ndi Mtima Wonse”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yos 12:7-24 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. M’pempheni kuti muziphunzira naye Baibulo pogwiritsa ntchito kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 6)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. M’patseni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale ndipo yambitsani phunziro la Baibulo mu phunziro 01. (th phunziro 20)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lffi phunziro 01 mfundo 5 (th phunziro 18)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (5 min.)
“Muzikumbukira Yehova Nthawi Zonse”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzigwira Ntchito ndi Moyo Wonse Ngati Kuti Mukugwirira Yehova.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 6 ndime 12-19
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 35 ndi Pemphero