CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Zimene Tikuphunzira pa Nkhani ya Agibeoni
Agibeoni anachita zinthu mwanzeru (Yos 9:3-6; it-1 930-931)
Akulu a ku Isiraeli anachita zinthu mopanda nzeru chifukwa sanafunsire malangizo kwa Yehova (Yos 9:14, 15; w11 11/15 8 ¶14)
Agibeoni ankatumikira Aisiraeli modzichepetsa (Yos 9:25-27; w04 10/15 18 ¶14)
Agibeoni anadzichepetsa n’kumagwira ntchito zonyozeka chifukwa ankafuna kuti Yehova aziwakonda. Kodi ifeyo tingatani kuti tizichita zinthu modzichepetsa?