September 13-19
YOSWA 1-2
Nyimbo Na. 97 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Zimene Mungachite Kuti Zinthu Zizikuyenderani Bwino”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Yos 2:4, 5—N’chifukwa chiyani Rahabi anapusitsa anthu omwe mfumu inawatuma kuti akafufuze azondi? (w04 12/1 8 ¶6)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yos 2:1-16 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Ulendo Wobwereza: Baibulo—Yob 26:7. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.
Ulendo Wobwereza: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza. (th phunziro 11)
Ulendo Wobwereza: (5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako m’patseni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale ndipo yambitsani phunziro la Baibulo. (th phunziro 16)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Pitirizani Kuphunzitsa Mphamvu Zanu za Kuzindikira”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti “Khalani ndi Chikumbumtima Chabwino.”
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 4 ndime 18-21, mfundo za m’Baibulo tsa. 56-59
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 124 ndi Pemphero