CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Tizidalira Yehova Kuti Atilimbikitse
Eliya anachita mantha ndipo anathawa kuti apulumutse moyo wake (1Mf 19:3, 4; w19.06 15 ¶5)
Yehova anamuthandiza Eliya ndipo anamusonyeza mphamvu zake m’njira zodabwitsa kwambiri (1Mf 19:5-7, 11, 12; ia 103 ¶13; 106 ¶21)
Yehova anamupatsa ntchito yoti agwire (1Mf 19:15-18; ia 106 ¶22)
Masiku ano, Yehova amatilankhula kudzera m’Mawu ake ndipo amatikumbutsa kuti amatikonda komanso kuti anatipatsa utumiki wofunika kwambiri woti tichite.—1Ak 15:58; Akl 3:23.