October 17-23
1 MAFUMU 21-22
Nyimbo Na. 134 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Muzitsanzira Mmene Yehova Amagwiritsira Ntchito Udindo Wake”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
1Mf 21:27-29—Kodi tikudziwa bwanji kuti zochita za Ahabu sizinasonyeze kuti analapa kuchokera pansi pamtima? (w21.10 3 ¶4-6)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Mf 22:24-38 (th phunziro 2)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. M’pempheni kuti muziphunzira naye Baibulo pogwiritsa ntchito kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 4)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale ndipo yambitsani phunziro la Baibulo pogwiritsa ntchito phunziro 01. (th phunziro 6)
Nkhani: (5 min.) w15 3/15 9-11 ¶10-12—Mutu: Kodi Tikuphunzira Chiyani pa Kukhulupirika kwa Naboti? (th phunziro 14)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Chikondi N’choleza Mtima Ndiponso N’chokoma Mtima”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani omvera mafunso otsatirawa: Kodi a Alexandru anasonyeza bwanji kuleza mtima komanso kukoma mtima monga mutu wa banja? N’chifukwa chiyani a Dorina anasintha n’kupita kwa nthawi? Kodi tikuphunzira chiyani pa zimene zinachitikira banjali?
Zofunika Pampingo: (5 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 23
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 50 ndi Pemphero