October 24-30
2 MAFUMU 1-2
Nyimbo Na. 79 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Chitsanzo Chabwino cha Kuphunzitsa Ena”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
2Mf 2:11—Kodi Eliya anapita kuti atatengedwa “mumphepo yamkuntho n’kukwera kumwamba”? (w05 8/1 9 ¶1)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mf 2:1-10 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 12)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mufotokozereni kuti timaphunzira Baibulo ndi anthu ndipo m’patseni khadi lodziwitsa anthu za phunziro la Baibulo. (th phunziro 13)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 07 zomwe taphunzira, kubwereza komanso zolinga (th phunziro 14)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Zinthu Zothandiza Zomwe Zili M’buku Lakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Funsani mwachidule wofalitsa mmodzi amene akuchititsa phunziro la Baibulo pogwiritsa ntchito buku la Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale: Kodi n’chiyani chimakusangalatsani mukamagwiritsa ntchito bukuli? Kodi mavidiyo komanso mafunso akuthandiza bwanji wophunzira wanu?
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 24
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 66 ndi Pemphero