CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Chitsanzo Chabwino cha Kuphunzitsa Ena
[Onerani vidiyo ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 2 Mafumu.]
Elisa ankaona pamene Eliya ankachita chozizwitsa (2Mf 2:8; w15 4/15 13 ¶15; onani chithunzi chapachikuto)
Modzichepetsa, Elisa anagwiritsa ntchito zomwe anaphunzitsidwa (2Mf 2:13, 14; w15 4/15 13 ¶16)
Yehova anapereka udindo kwa akulu mumpingo woti aziphunzitsa ena. (2Ti 2:2) Akulu akamakuphunzitsani, muzikhala wofunitsitsa, wodalirika komanso wodzichepetsa.