October 31–November 6
2 MAFUMU 3-4
Nyimbo Na. 151 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Nyamulani Mwana Wanu”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
2Mf 4:38—Kodi n’kutheka kuti “ana a aneneri” anali ndani? (it-2 697 ¶2)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mf 3:1-12 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 17)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? (th phunziro 20)
Nkhani: (5 min.) w13 8/15 28-29—Mutu: Kodi Mungatsanzire Bwanji Elisa pa Nkhani ya Kudzichepetsa Mukamachita Utumiki Wopatulika? (th phunziro 15)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Kufikira Pamene Adzakhalenso Ndi Moyo”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Zimene Mungachite Mukaferedwa.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 25
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 139 ndi Pemphero