CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kukhala Okhutira Komanso Odzichepetsa?
Mneneri wa Mulungu anakana kulandira mphatso zapamwamba za Yerobowamu (1Mf 13:7-10; w08 8/15 8 ¶4)
Pambuyo pake mneneriyo anaphwanya lamulo lachindunji la Yehova (1Mf 13:14-19; w08 8/15 11 ¶15)
Kusamvera kwa mneneriyu kunamubweretsera mavuto (1Mf 13:20-22; w08 8/15 9 ¶10)
Tikakhala okhutira n’kumadalira Yehova posankha zochita, tikhoza kupewa mavuto ambiri.—1Ti 6:8-10
DZIFUNSENI KUTI: ‘Kodi ndingasonyeze bwanji kuti ndine wokhutira ndi zinthu zofunika zimene ndili nazo? Kodi ndingasonyeze bwanji kuti ndine wodzichepetsa ndikamasankha zochita?’—Miy 3:5; 11:2.