October 2-8
YOBU 1-3
Nyimbo Na. 141 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Pitirizani Kusonyeza Kuti Mumakonda Kwambiri Yehova”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Yob 1:10—Kodi lembali likutithandiza bwanji kumvetsa mawu a Yesu opezeka pa lemba la Mateyu 27:46? (w21.04 11 ¶9)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yob 3:1-26 (th phunziro 12)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako mufotokozereni za webusaiti yathu ya jw.org, ndipo mugawireni khadi lodziwitsa anthu za webusaitiyi. (th phunziro 9)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo?, kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 20)
Nkhani: (5 min.) w22.01 11-12 ¶11-14—Mutu: Tiziphunzitsa Mogwira Mtima Ngati Yakobo—Tizipereka Malangizo Mosapita M’mbali Komanso Tizikhala Odzichepetsa. (th phunziro 18)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Ndinkaganiza Ngati Ndili Ndi Chilichonse: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani mafunso otsatirawa: N’chifukwa chiyani M’bale Birdwell ankaganiza kuti anali ndi chilichonse?
Kodi kuganizira mfundo ya pa lemba la Mateyu 6:33 kunathandiza bwanji m’baleyu?
Kodi mwaphunzirapo chiyani pa chitsanzo cha banja la a Birdwell?
“Muzigwiritsa Ntchito Tsamba Loyamba la JW.ORG Mukakhala mu Utumiki”: (5 min.) Nkhani yokambirana.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 59 mfundo 6 komanso zomwe taphunzira, kubwereza ndi zolinga
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 129 ndi Pemphero