Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Pitirizani Kusonyeza Kuti Mumakonda Kwambiri Yehova

Pitirizani Kusonyeza Kuti Mumakonda Kwambiri Yehova

[Onerani vidiyo ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Yobu.]

Satana ankanena kuti Yobu ankatumikira komanso kukonda Yehova chifukwa cha dyera (Yob 1:​8-11; w18.02 6 ¶16-17)

Satana amanena kuti ifenso sitikonda Yehova ndi mtima wonse (Yob 2:​4, 5; w19.02 5 ¶10)

Yehova anapereka mwayi kwa tonsefe woti tizisonyeza kuti Satana ndi wabodza. (Miy 27:11) Tingasonyeze kuti timakonda kwambiri Yehova pochita zinthu zomusangalatsa kaya zinthu zili bwino pa moyo wathu kapena ayi.