CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Njira Zitatu Zomwe Tingapezere Nzeru N’kumazigwiritsa Ntchito
Muzichita chidwi ndi zinthu zam’chilengedwe (Yob 12:7-9; w09 4/15 6 ¶17)
Muzikhala pa ubwenzi ndi Akhristu okhulupirika (Yob 12:12; w21.06 10 ¶10-12)
Muziphunzira mfundo za Mulungu ndipo muzizigwiritsa ntchito pa moyo wanu (Yob 12:16; it-2 1190 ¶2)
DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndaphunzira chiyani chifukwa chocheza ndi Akhristu okhulupirika?