CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Samalani ndi Nkhani Zabodza
Zimene Elifazi ankanena zinkaoneka ngati zoona chifukwa anali wamkulu komanso wanzeru (Yob 4:1; it-1 713 ¶11)
Ziwanda zinamutsogolera kuti akapereke uthenga wofooketsa kwa Yobu (Yob 4:14-16; w05 9/15 26 ¶2)
Zina mwa zomwe Elifazi ananena zinali zoona, koma anazigwiritsa ntchito molakwika (Yob 4:19; w10 2/15 19 ¶5-6)
Dziko la Satanali limafalitsa nkhani zabodza zowononga.
DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndimapeza nthawi yoti nditsimikizire kaye ngati nkhani zimene ndikumva kapena kuwerenga zilidi zoona?’—mrt 32 ¶13-17