September 11-17
ESITERE 3-5
Nyimbo Na. 85 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Muzithandiza Ena Kuti Azichita Zambiri”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Est 4:12-16—Kodi timamenyera bwanji ufulu wolambira ngati mmene Esitere ndi Moredekai anachitira? (kr 160 ¶14)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Est 3:1-12 (th phunziro 2)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo ya Ulendo Wobwereza: Ufumu—Mt 14:19, 20. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.
Ulendo Wobwereza: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Muuzeni kuti timaphunzira Baibulo ndi anthu ndipo musiyireni khadi lodziwitsa anthu za phunziro la Baibulo. (th phunziro 16)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 12 mawu oyamba komanso mfundo 1-3 (th phunziro 15)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Khalani Bwenzi la Yehova—Nditsanzire Esitere: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako ngati n’zotheka funsani ana omwe munawasankhiratu funso ili: Kodi mungatsanzire bwanji kulimba mtima kwa Esitere?
Zofunika Pampingo: (10 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 57
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 125 ndi Pemphero