September 25–October 1
ESITERE 9-10
Nyimbo Na. 102 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Anagwiritsa Ntchito Udindo Wake Pothandiza Anthu Ena”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Est 9:15, 16—N’chifukwa chiyani Ayuda sanatenge zofunkha? (w06 3/1 11 ¶4)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Est 9:1-14 (th phunziro 11)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (2 min.) Gwiritsani ntchito nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 6)
Ulendo Wobwereza: (5 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, ndipo musonyezeni mmene phunziro la Baibulo limachitikira. (th phunziro 13)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 12 mawu oyamba a pa Fufuzani Mozama ndi mfundo 4 (th phunziro 19)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Abusa Amene Amachitira Zabwino Anthu a Yehova”: (15 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 59 mfundo 1-5
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 55 ndi Pemphero