October 14-20
MASALIMO 96-99
Nyimbo Na. 66 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)
1. “Muzilengeza Uthenga Wabwino”
(10 min.)
Muziuza ena uthenga wabwino (Sl 96:2; w11 3/1 6 ¶1-2)
Muziwaphunzitsa za uthenga wabwino wonena za Tsiku la Chiweruzo (Sl 96:12, 13; w12 9/1 16 ¶1)
Muziwathandiza kudziwa cholinga cha Yehova choti padziko lapansi padzaze anthu amene amatamanda dzina lake (Sl 99:1-3; w12 9/15 12 ¶18-19)
2. Mfundo Zothandiza
(10 min.)
Sl 96:1—Kodi mawu akuti “nyimbo yatsopano” amanena za chiyani m’malo ambiri amene mawuwa akupezeka? (it-2 994)
Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
3. Kuwerenga Baibulo
(4 min.) Sl 98:1–99:9 (th phunziro 11)
4. Kudzipereka—Zomwe Yesu Anachita
(7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani VIDIYO, kenako kambiranani lmd phunziro 10 mfundo 1-2.
5. Kudzipereka—Zomwe Mungachite Potsanzira Yesu
(8 min.) Nkhani yokambirana kuchokera mu kabuku ka lmd phunziro 10 mfundo 3-5 ndi “Onaninso Malemba Awa.”
Nyimbo Na. 9
6. Zofunika Pampingo
(15 min.)
7. Phunziro la Baibulo la Mpingo
(30 min.) bt mutu 16 ¶10-18