October 21-27
MASALIMO 100-102
Nyimbo Na. 37 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)
1. Muziyamikira Chikondi Chokhulupirika cha Yehova
(10 min.)
Muzikonda kwambiri Yehova (Sl 100:5; w23.03 12 ¶18-19)
Muzipewa zinthu zimene zingawononge ubwenzi wanu ndi Yehova (Sl 101:2, 3; w23.02 17 ¶10)
Muzipewa anthu amene amanena zabodza zokhudza Yehova ndi gulu lake (Sl 101:5; w11 7/15 16 ¶7-8)
DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndikhoza kuwononga ubwenzi wanga ndi Yehova chifukwa cha mmene ndimagwiritsira ntchito intaneti?’
2. Mfundo Zothandiza
(10 min.)
Sl 102:6—N’chifukwa chiyani wolemba salimoli anadziyerekezera ndi mbalame yotchedwa vuwo? (it-2 596)
Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
3. Kuwerenga Baibulo
(4 min.) Sl 102:1-28 (th phunziro 12)
4. Ulendo Woyamba
(3 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. (lmd phunziro 2 mfundo 3)
5. Ulendo Wobwereza
(5 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. M’pempheni kuti muziphunzira naye Baibulo. (lmd phunziro 9 mfundo 4)
6. Kufotokoza Zimene Mumakhulupirira
(4 min.) Chitsanzo. ijwbq 129—Mutu: Kodi Baibulo Linasinthidwa Kapena Kusokonezedwa? (th phunziro 8)
Nyimbo Na. 137
7. ‘Ndikumamatirani, Inuyo Mundigwire Mwamphamvu’
(15 min.)
Nkhani yokambirana. Onerani VIDIYO. Kenako funsani mafunso awa:
Kodi Anna anasonyeza bwanji chikondi chokhulupirika?
Kodi tingamutsanzire bwanji?
8. Phunziro la Baibulo la Mpingo
(30 min.) bt mutu 17 ¶1-7