Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

September 30–October 6

MASALIMO 90-91

September 30–October 6

Nyimbo Na. 140 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. Muzikhulupirira Yehova Kuti Mukhale ndi Moyo Wautali

(10 min.)

N’zosatheka kuti anthufe patokha titalikitse moyo wathu (Sl 90:10; wp19.3 5 ¶3-5)

Yehova ndi “Mulungu kuyambira kalekale mpaka kalekale” (Sl 90:2; wp19.1 5, bokosi)

Akhoza kupereka ndipo adzapereka moyo wosatha kwa anthu amene amamukhulupirira (Sl 21:4; 91:16)

Musasokoneze ubwenzi wanu ndi Yehova polola thandizo la mankhwala lomwe ndi losemphana ndi mfundo zake.—w22.06 18 ¶16-17.

2. Mfundo Zothandiza

(10 min.)

  • Sl 91:11—Kodi tiziliona bwanji thandizo limene angelo amapereka? (wp17.5 5)

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

3. Kuwerenga Baibulo

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

4. Ulendo Woyamba

(3 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Popanda kukambirana za Baibulo, chezani ndi munthuyo m’njira yoti mudziwe mmene Baibulo lingamuthandizire pa moyo wake. (lmd phunziro 1 mfundo 3)

5. Ulendo Woyamba

(4 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. (lmd phunziro 1 mfundo 4)

6. Nkhani

(5 min.) lmd zakumapeto A mfundo 5—Mutu: Mungathe Kudzakhala Ndi Moyo Padzikoli Mpaka Kalekale. (th phunziro 14)

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Nyimbo Na. 158

7. Muzisangalala Ndi Kuleza Mtima kwa Mulungu—Mmene Yehova Amaonera Nthawi

(5 min.) Nkhani yokambirana.

Onerani VIDIYO. Kenako funsani funso ili:

  • Kodi kuganizira mmene Yehova amaonera nthawi kungatithandize bwanji kuti tiziyembekezera malonjezo ake moleza mtima?

8. Vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya September

(10 min.) Onerani VIDIYOYI.

9. Phunziro la Baibulo la Mpingo

Mawu Omaliza (3 min.) | Nyimbo Na. 68 ndi Pemphero