“Nthawi Yodikira Yatha”
Onani mmene kukwaniritsidwa kwa maulosi ochititsa chidwi a m’buku la Chivumbulutso kudzathandizire kuti padzikoli pakhale chilungamo komanso mtendere kwa anthu amene amakonda Yehova. Nkhaniyi yachokera pa Chivumbulutso 18:1–19:3; 19:11–20:3; 20:12-14; 22:1-7.