“Yehova Anawachititsa Kusangalala”
Vidiyoyi ikusonyeza mmene kulimba mtima komanso chikhulupiriro zinathandizira Zerubabele, Yoswa yemwe anali Mkulu wa Ansembe komanso Ayuda amene anachoka ku ukapolo, kukhalabe osangalala ngakhale kuti ankatsutsidwa kwambiri. Nkhaniyi yachokera pa Ezara 1:1-6; 3:1-6, 10-13; 4:1-7, 11-16; 5:3-5; 6:6-12, 22; Hagai 1:2-11; 2:3-9; Zekariya 1:12-16; 2:7-9; 3:1, 2; 4:6, 7.