Mabuku Ophunzirira Baibulo
Phunzirani Baibulo m’njira yotsatira mutu ndi mutu, pogwiritsa ntchito mabuku amenewa omwe mungathe kuwakopera pa Intaneti.
Sankhani chinenero chimene mukufuna pa kabokosi ka zinenero, kenako dinani kabatani ka Fufuzani kuti muone mabuku ndi timabuku tomwe tilipo m’chinenerocho. Lembani mawu amodzi kapena awiri a dzina la buku kapena kabuku kamene mukufuna.