Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2019
Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa Mboni za Yehova wa 2019 wakuti “Chikondi Sichitha.”
Lachisanu
Pulogalamu ya Lachisanu yachokera pa 1 Atesalonika 4:9—‘Mulungu amatiphunzitsa kukondana.’
Loweruka
Pulogalamu ya Loweruka yachokera pa Aefeso 5:2—“Yendanibe m’chikondi.”
Lamlungu
Pulogalamu ya Lamlungu yachokera pa Yuda 21—“Pitirizani kuchita zinthu zimene zingachititse Mulungu kukukondani.”
Mawu kwa Osonkhana
Dziwani zoyenera kuchita pa msonkhano wachigawo.