Loweruka
“YENDANIBE M’CHIKONDI”—AEFESO 5:2
M’MAWA
-
9:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
-
9:30 Nyimbo Na. 85 ndi Pemphero
-
9:40 NKHANI YOSIYIRANA: Muzisonyeza Chikondi Chosatha Mumpingo Wachikhristu
-
Muzikonda Amene Akutitsogolera (1 Atesalonika 5:12, 13)
-
Muzikonda Akazi Amasiye ndi Ana Amasiye (Yakobo 1:27)
-
Muzikonda Achikulire (Levitiko 19:32)
-
Muzikonda Amene Akuchita Utumiki wa Nthawi Zonse (1 Atesalonika 1:3)
-
Muzikonda Anthu Ochokera Kumayiko Ena (Levitiko 19:34; Aroma 15:7)
-
-
10:50 Nyimbo Na. 58 ndi Zilengezo
-
11:00 NKHANI YOSIYIRANA: Muzisonyeza Chikondi Chosatha mu Utumiki
-
Muzisonyeza Kuti Mumakonda Mulungu (1 Yohane 5:3)
-
“Uzikonda Mnzako Mmene Umadzikondera Wekha” (Mateyu 22:39)
-
Muzikonda Mawu a Yehova (Salimo 119:97; Mateyu 13:52)
-
-
11:45 NKHANI YA UBATIZO: Phunzirani Kukonda Ena Kuchokera kwa Yesu (Mateyu 11:28-30)
-
12:15 Nyimbo Na. 52 ndi Kupuma
MASANA
-
1:35 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
-
1:45 Nyimbo Na. 84
-
1:50 NKHANI YOSIYIRANA: Mmene Abale Athu Akusonyezera Chikondi Chimene Sichitha
-
Ku Africa (Genesis 16:13)
-
Ku Asia (Machitidwe 2:44)
-
Ku Europe (Yohane 4:35)
-
Ku North America (1 Akorinto 9:22)
-
Ku Oceania (Salimo 35:18)
-
Ku South America (Machitidwe 1:8)
-
-
2:55 NKHANI YOSIYIRANA: Muzisonyeza Chikondi Chosatha M’banja
-
Muzikonda Mkazi Wanu (Aefeso 5:28, 29)
-
Muzikonda Mwamuna Wanu (Aefeso 5:33; 1 Petulo 3:1-6)
-
Muzikonda Ana Anu (Tito 2:4)
-
-
3:35 Nyimbo Na. 35 ndi Zilengezo
-
3:45 VIDIYO: Nkhani ya Yosiya Imatiphunzitsa Kukonda Yehova Komanso Kudana ndi Zoipa—Mbali Yoyamba (2 Mbiri 33:10-24; 34:1, 2)
-
4:15 Muziphunzitsa Ana Anu Mmene Angasonyezere Chikondi (2 Timoteyo 3:14, 15)
-
4:50 Nyimbo Na. 134 ndi Pemphero Lomaliza