Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
1. N’chifukwa chiyani tiyenera kulimbitsa chikhulupiriro chathu panopa? (Aheb. 10:39)
2. Kodi “tingaone” bwanji Yehova ngakhale kuti iye ndi wosaoneka? (Aheb. 11:27)
3. N’chifukwa chiyani n’zofunika kuti tiziphunzira maulosi a m’Baibulo? (Aroma 10:17)
4. Kodi mzimu woyera ungatithandize bwanji kuti tikhale ndi chikhulupiriro? (Luka 11:13; Agal. 5:22)
5. Kodi tingathandize bwanji ena kukhala ndi chikhulupiriro cholimba? (1 Ates. 2:7, 8)
6. N’chifukwa chiyani tiyenera kuyang’anitsitsa “Mtumiki Wamkulu ndi Wokwaniritsa chikhulupiriro chathu”? (Aheb. 12:2, 3)