Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Khalani ndi ‘Chikhulupiriro.’

Khalani ndi ‘Chikhulupiriro.’

YOHANE 14:1

M’MAWA

  • 9:30 Kumvetsera Nyimbo

  • 9:40 Nyimbo Na. 118 ndi Pemphero

  • 9:50 Mmene Tingasonyezere Kuti ‘Timakhulupirira’ Ndiponso Chifukwa Chake

  • 10:05 Nkhani Yosiyirana: Muzitsanzira Anthu Amene Anasonyeza Chikhulupiriro

    • • Isaki ndi Rabeka

    • • Esitere

    • • Timoteyo

  • 11:05 Nyimbo Na. 60 ndi Zilengezo

  • 11:15 ‘Tili ndi Chikhulupiriro, Chotero Timalankhula’

  • 11:30 Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa

  • 12:00 Nyimbo Na. 52

MASANA

  • 1:10 Kumvetsera Nyimbo

  • 1:20 Nyimbo Na. 9 ndi Pemphero

  • 1:30 Nkhani ya Baibulo ya Onse: Muzikhulupirira Mulungu “Amene Sanganame”

  • 2:00 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda

  • 2:30 Nyimbo Na. 54 ndi Zilengezo

  • 2:40 Nkhani Yosiyirana: ‘Muziyenda mwa Chikhulupiriro’ Tsiku Lililonse

    • • “Musamade Nkhawa”

    • • “Muzigwiritsa Ntchito Bwino Nthawi Yanu”

    • • Musamakhale “Mbali ya Dziko”

  • 3:40 “Yehova Amadziwa Anthu Ake”

  • 4:15 Nyimbo Na. 7 ndi Pemphero