Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Pezani Mayankho a Mafunso Awa

Pezani Mayankho a Mafunso Awa
  1. 1. Kodi chidzachitike n’chiyani tikamasonyeza chikhulupiriro? (Yoh. 3:16)

  2. 2. Kodi tingatsanzire bwanji chikhulupiriro cha Isaki ndi Rabeka, Esitere komanso Timoteyo? (Mlal. 4:11, 12; Sal. 119:46; 2 Tim. 1:5)

  3. 3. N’chiyani chingatithandize kuti tizipitirizabe kulalikira ngakhale tikumane ndi mavuto? (2 Akor. 4:13)

  4. 4. Kodi tingatani kuti ‘tiziyenda mwachikhulupiriro’ tsiku lililonse? (2 Akor. 5:7)

  5. 5. Kodi tingatani kuti Yehova azitidziwa? (2 Tim. 2:19; Yak. 4:6; 2 Akor. 13:5)