Pulogalamu ya Msonkhano wa 2021
Lachisanu
Pulogalamu ya Lachisanu yachokera pa Luka 17:5—“Tiwonjezereni chikhulupiriro.”
Loweruka
Pulogalamu ya Loweruka yachokera pa Yuda 3—‘Menya mwamphamvu nkhondo yachikhulupiriro.’
Lamlungu
Pulogalamu ya Lamlungu yachokera pa Mateyu 21:21—“Ngati mutakhala ndi chikhulupiriro . . . , zidzachitikadi.”
Mawu kwa Osonkhana
Mawu othandiza anthu amene abwera pamsonkhano.