Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Anthu Okonda Mtendere

Anthu Okonda Mtendere

LUKA 10:6

M’mawa

  • 9:40 Kumvetsera Nyimbo

  • 9:50 Nyimbo Na. 58 ndi Pemphero

  • 10:00 Takulandirani Anthu Okonda Mtendere

  • 10:15 Pitirizani Kufufuza Anthu Okonda Mtendere

  • 10:30 Muzilola Kuti Kalonga Wamtendere Akuthandizeni Kufufuza Anthu Okonda Mtendere

  • 10:55 Nyimbo Na. 103 ndi Zilengezo

  • 11:05 Anthu Okonda Mtendere Saphunzira Nkhondo

  • 11:35 Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa

  • 12:05 Nyimbo Na. 79

Masana

  • 1:20 Kumvetsera Nyimbo

  • 1:30 Nyimbo Na. 76

  • 1:35 Zochitika pa Moyo Wachikhristu

  • 1:45 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda

  • 2:15 Nkhani Yosiyirana: Anthu Okonda Mtendere Amathandizana

    • • “Muzifutukula Mtima Wanu”

    • • Muzithandiza Achinyamata Kuti Azichita Zambiri

    • • Muzilemekeza Achikulire

  • 3:00 Nyimbo Na. 57 ndi Zilengezo

  • 3:10 Mmene Anthu Okonda Mtendere Amagonjetsera Choipa Pochita Chabwino

  • 3:55 Nyimbo Na. 45 ndi Pemphero