Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Banja la Yehova Logwirizana

Banja la Yehova Logwirizana

AEFESO 4:3

M’mawa

  • 9:30 Kumvetsera Nyimbo

  • 9:40 Nyimbo Na. 85 ndi Pemphero

  • 9:50 Muziyamikira Mwayi Wanu Wokhala M’banja la Yehova

  • 10:05 Nkhani Yosiyirana: Anathandiza Kuti Ena Azimva Bwino

    • • Elihu

    • • Lidiya

    • • Yesu

  • 11:05 Nyimbo Na. 100 ndi Zilengezo

  • 11:15 Pitirizani Kuthandiza Ena Kuti Akhale M’banja la Yehova

  • 11:30 Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa

  • 12:00 Nyimbo Na. 135

Masana

  • 1:10 Kumvetsera Nyimbo

  • 1:20 Nyimbo Na. 132 ndi Pemphero

  • 1:30 Nkhani ya Baibulo ya Onse: Kodi Panyumba Panu Ndi Malo a Mpumulo Ndi Mtendere?

  • 2:00 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda

  • 2:30 Nyimbo Na. 136 ndi Zilengezo

  • 2:40 Nkhani Yosiyirana: Muzilimbikitsa Mtendere

    • • Muzilankhula ‘Mawu Olimbikitsa’

    • • ‘Muziyenda M’chikondi’

    • • Muzipewa Adani Athu

  • 3:40 ‘Tisamaleke Kuyamika Mulungu’ Chifukwa cha Abale ndi Alongo Athu

  • 4:15 Nyimbo Na. 107 ndi Pemphero