Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mupeze Mayankho a Mafunso Awa

Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
  1. 1. Kodi tingasonyeze bwanji kuti timayamikira malo omwe tili nawo m’banja la Yehova? (Aef. 4:3)

  2. 2. Kodi tingatani kuti tizichititsa ena kuti azimva bwino, nanga tingachite bwanji zimenezi? (Aroma 15:7)

  3. 3. Kodi tingatani kuti tithandize anthu ambiri kuti abwere m’banja la Yehova? (Aef. 2:17; 6:15)

  4. 4. Kodi tingatani kuti tikhale anthu olimbikitsa mtendere? (Aef. 4:29; 5:1, 2; 6:13)

  5. 5. Kodi tingatani kuti tizikonda kwambiri abale ndi alongo athu? (Aef. 1:15, 16)

© 2022 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

CA-copgm23-CN