Lachisanu
M’Mawa
-
9:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
-
9:30 Nyimbo Na. 86 ndi Pemphero
-
9:40 NKHANI YA TCHEYAMANI: Yehova Ndi “Mulungu Amene Amapatsa Mtendere” (Aroma 15:33; Afilipi 4:6, 7)
-
10:10 NKHANI YOSIYIRANA: Chikondi Chimatithandiza Kukhala ndi Mtendere Weniweni
-
• Kukonda Mulungu (Mateyu 22:37, 38; Aroma 12:17-19)
-
• Kukonda Anzathu (Mateyu 22:39; Aroma 13:8-10)
-
• Kukonda Mawu a Mulungu (Salimo 119:165, 167, 168)
-
-
11:05 Nyimbo Na. 24 ndi Zilengezo
-
11:15 KUWERENGA BAIBULO MWASEWERO: Yakobo Anali Munthu Wokonda Mtendere (Genesis 25:21–33:11)
-
11:45 “Ntchito ya Chilungamo Chenicheni Idzakhala Mtendere” (Yesaya 32:17; 60:21, 22)
-
12:15 Nyimbo Na. 97 ndi Kupuma
Masana
-
1:35 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
-
1:45 Nyimbo Na. 144
-
1:50 NKHANI YOSIYIRANA: Tizisangalala ndi Malonjezo a Mulungu Okhudza Mtendere
-
• “Atumiki Anga Adzadya . . . Atumiki Anga Adzamwa” (Yesaya 65:13, 14)
-
• “Iwo Adzamanga Nyumba . . . Adzabzala Minda ya Mpesa” (Yesaya 65:21-23)
-
• “Mmbulu ndi Mwana wa Nkhosa Zidzadyera Pamodzi” (Yesaya 11:6-9; 65:25)
-
• “Palibe . . . Amene Adzanene Kuti: ‘Ndikudwala.’” (Yesaya 33:24; 35:5, 6)
-
• “Iye Adzameza Imfa Kwamuyaya” (Yesaya 25:7, 8)
-
-
2:50 Nyimbo Na. 35 ndi Zilengezo
-
3:00 NKHANI YOSIYIRANA: Zimene Zingathandize Kuti M’banja Muzikhala Mtendere
-
• Muzikondana Komanso Kulemekezana (Aroma 12:10)
-
• Muzilankhulana Nthawi Zonse (Aefeso 5:15, 16)
-
• Muzichita Zinthu Mogwirizana (Mateyu 19:6)
-
• Muzilambira Yehova Limodzi (Yoswa 24:15)
-
-
3:55 Muzithandiza “Kalonga Wamtendere” Mokhulupirika (Yesaya 9:6, 7; Tito 3:1, 2)
-
4:15 Tisamapusitsidwe ndi Mtendere Wosakhalitsa (Mateyu 4:1-11; Yohane 14:27; 1 Atesalonika 5:2, 3)
-
4:50 Nyimbo Na. 112 ndi Pemphero Lomaliza