Lamlungu
M’Mawa
-
9:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
-
9:30 Nyimbo Na. 101 ndi Pemphero
-
9:40 NKHANI YOSIYIRANA: Anafesa ndi Kukolola Mtendere
-
• Yosefe ndi Abale Ake (Agalatiya 6:7, 8; Aefeso 4:32)
-
• Agibiyoni (Aefeso 5:17)
-
• Gidiyoni (Oweruza 8:2, 3)
-
• Abigayeli (1 Samueli 25:27-31)
-
• Mefiboseti (2 Samueli 19:25-28)
-
• Paulo ndi Baranaba (Machitidwe 15:36-39)
-
• Akhristu a Masiku Ano (1 Petulo 2:17)
-
-
11:05 Nyimbo Na. 28 ndi Zilengezo
-
11:15 NKHANI YA ONSE: Kodi Mungatani Kuti Mukhale pa Ubwenzi ndi Mulungu? (Yakobo 4:8; 1 Yohane 4:10)
-
11:45 Nyimbo Na. 147 ndi Kupuma
Masana
-
1:35 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
-
1:45 Nyimbo Na. 23
-
1:50 VIDIYO YA NKHANI YA M’BAIBULO: Yehova Amatitsogolera Panjira Yamtendere—Mbali Yachiwiri (Yesaya 48:17, 18)
-
2:30 Nyimbo Na. 139 ndi Zilengezo
-
2:40 Chilengedwe Chonse Chidzakhala Pamtendere (Aroma 16:20; 1 Akorinto 15:24-28; 1 Yohane 3:8)
-
3:40 Nyimbo Yatsopano Komanso Pemphero Lomaliza