Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mawu kwa Osonkhana

Mawu kwa Osonkhana

Ubatizo Akulu amumpingo wanu akonza dongosolo labwino mogwirizana ndi mmene zinthu zilili m’dera lanu kuti anthu amene akufuna kubatizidwa, adzabatizidwe Loweruka chigawo cha m’mawa chikatha.

Zopereka Msonkhanowu wamasuliridwa m’zilankhulo zoposa 500. Ndalama zimene mumapereka mwa kufuna kwanu ndi zimene zimathandiza pa ntchitoyi yomwe ikuchitika padziko lonse. Mungapereke ndalama kudzera pa intaneti pogwiritsa ntchito donate.pr418.com. Timayamikira kwambiri zopereka zanu, ndipo Bungwe Lolamulira likukuyamikirani chifukwa chothandiza ndi mtima wonse pa ntchito ya Ufumu.

Wakonzedwa ndi Bungwe Lolamulira la Mboni za Yehova

© 2022 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania