Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mupeze Mayankho a Mafunso Awa

Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
  1. 1. N’chifukwa chiyani ‘sitichita manyazi ndi uthenga wabwino’? (Aroma 1:16; 11:13)

  2. 2. Kodi timasonyeza bwanji kuti tili kumbali ya choonadi? (Mat. 10:32; Aroma 10:9)

  3. 3. Kodi n’chiyani chimatithandiza kuti tizilalikira bwino tikakhala mu utumiki? (2 Tim. 2:15)

  4. 4. Kodi tingatsanzire bwanji Onesiforo? (2 Tim. 1:​7, 8)

  5. 5. Kodi timasonyeza bwanji kuti sitichita manyazi kukhala kumbali ya Mulungu wathu? (Aheb. 10:39; 1 Pet. 3:15; Yoh. 18:36; 1 Ates. 5:​12, 13)

  6. 6. Kodi ‘timadzitama bwanji mwa Yehova’? (Sal. 34:​1, 2; 1 Akor. 1:31)

© 2024 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

CA-brpgm25-CN