Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

‘Sitichita Manyazi ndi Uthenga Wabwino’

‘Sitichita Manyazi ndi Uthenga Wabwino’

AROMA 1:​16

M’mawa

  • 9:40 Kumvetsera Nyimbo

  • 9:50 Nyimbo Na. 67 ndi Pemphero

  • 10:00 N’chifukwa Chiyani ‘Sitichita Manyazi ndi Uthenga Wabwino’?

  • 10:15 Muzilalikira Molimba Mtima Uthenga Wabwino

  • 10:30 Mukhale “Munthu Wosachita Manyazi ndi Ntchito Imene Wagwira”

  • 10:55 Nyimbo Na. 73 ndi Zilengezo

  • 11:05 Muzisonyeza Kuti Ndinu Wamphamvu, Wachikondi Komanso Woganiza Bwino

  • 11:35 Nkhani ya Ubatizo: Pitirizani ‘Kugonjera Uthenga Wabwino’

  • 12:05 Nyimbo Na. 75

Masana

  • 1:20 Kumvetsera Nyimbo

  • 1:30 Nyimbo Na. 77

  • 1:35 Zochitika pa Moyo wa Chikhristu

  • 1:45 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda

  • 2:15 Nkhani Yosiyirana: Sitichita Manyazi . . .

    • • Ndi Mfundo za Mulungu za Makhalidwe Abwino

    • • Ndi Ufumu wa Mulungu

    • • Ndi Anthu Amene Akutsogolera M’gulu la Mulungu

  • 3:00 Nyimbo Na. 40 ndi Zilengezo

  • 3:10 ‘Muzidzitama mwa Yehova’

  • 3:55 Nyimbo Na. 7 ndi Pemphero