Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

“Makhalidwe Anu Akhale Ogwirizana ndi Uthenga Wabwino”

“Makhalidwe Anu Akhale Ogwirizana ndi Uthenga Wabwino”

AFILIPI 1:​27

M’mawa

  • 9:40 Nyimbo

  • 9:50 Nyimbo Na. 35 ndi Pemphero

  • 10:00 Kodi Uthenga Wabwino Ukukuthandizani Kusintha?

  • 10:15 Nkhani Yosiyirana: Mmene Uthenga Wabwino Unawathandizira

    • • Sitefano

    • • Filipo

    • • Akula ndi Purisila

    • • Tito

  • 11:05 Nyimbo Na. 76 ndi Zilengezo

  • 11:15 Pitirizani ‘Kuchita Ntchito Zosonyeza Kuti Ndinu Odzipereka kwa Mulungu’

  • 11:35 Nkhani ya Ubatizo: Pitirizani ‘Kugonjera Uthenga Wabwino’

  • 12:05 Nyimbo Na. 37

Masana

  • 1:20 Nyimbo

  • 1:30 Nyimbo Na. 56 ndi Pemphero

  • 1:35 Nkhani ya Onse: N’chifukwa Chiyani Mumakhulupirira Zimene Mumakhulupirira?

  • 2:05 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda

  • 2:35 Nyimbo Na. 24 ndi Zilengezo

  • 2:45 Nkhani Yosiyirana: “Tikusonyeza M’njira Iliyonse Kuti Ndife Atumiki a Mulungu . . . ”

    • • Popirira

    • • Pokhala Okoma Mtima

    • • Pochita Zinthu Moona Mtima

  • 3:30 Kodi Uthenga Wabwino Umatiphunzitsa Chiyani?

  • 4:00 Nyimbo Na. 29 ndi Pemphero