4-B
Zochitika Zikuluzikulu m’Moyo wa Yesu Padziko Lapansi—Chiyambi cha Utumiki wa Yesu
NTHAWI |
MALO |
CHOCHITIKA |
MATEYU |
MALIKO |
LUKA |
YOHANE |
---|---|---|---|---|---|---|
29, chakumapeto kwa chaka |
Mtsinje wa Yorodano, mwina chapafupi kapena ku Betaniya wa kutsidya lina la Yorodano |
Ubatizo ndi kudzozedwa kwa Yesu; Yehova akulengeza kuti Yesu ndi Mwana wake ndipo akumuvomereza |
||||
Chipululu cha Yudeya |
Yesu ayesedwa ndi Mdyerekezi |
|||||
Betaniya wa kutsidya lina la Yorodano |
Yohane M’batizi akunena za Yesu monga Mwanawankhosa wa Mulungu; ophunzira oyamba akuyamba kutsatira Yesu |
|||||
Kana wa ku Galileya; Kaperenao |
Chozizwitsa choyamba cha Yesu, kusandutsa madzi kukhala vinyo; apita ku Kaperenao |
|||||
30, Pasika |
Yerusalemu |
Athamangitsa amalonda m’kachisi |
||||
Yesu akambirana ndi Nikodemo |
||||||
Yudeya; Ainoni |
Apita kumadera a kumidzi a ku Yudeya, ophunzira ake abatiza anthu; Ulaliki womalizira wa Yohane wokhudza Yesu |
|||||
Tiberiyo; Yudeya |
Yohane aponyedwa m’ndende; Yesu anyamuka kupita ku Galileya |
|||||
Sukari, ku Samariya |
Ulendo wa ku Galileya, aphunzitsa Asamariya |