4-C
Zochitika Zikuluzikulu M’moyo wa Yesu Padziko Lapansi—Utumiki Waukulu wa Yesu M’Galileya (Gawo 1)
NTHAWI |
MALO |
CHOCHITIKA |
MATEYU |
MALIKO |
LUKA |
YOHANE |
---|---|---|---|---|---|---|
30 |
Galileya |
Choyamba alengeza kuti “Ufumu wakumwamba wayandikira” |
||||
Kana; Nazareti; Kaperenao |
Achiritsa mnyamata; awerenga mpukutu wa Yesaya; akanidwa; apita ku Kaperenao |
|||||
Nyanja ya Galileya, pafupi ndi Kaperenao |
Aitana ophunzira anayi: Simoni ndi Andireya, Yakobo ndi Yohane |
|||||
Kaperenao |
Achiritsa apongozi a Simoni ndi ena |
|||||
Galileya |
Ulendo woyamba wozungulira mu Galileya ali ndi ophunzira anayi |
|||||
Wakhate achiritsidwa; anthu miyandamiyanda akhamukira kwa Yesu |
||||||
Kaperenao |
Achiritsa wakufa ziwalo |
|||||
Kuitanidwa kwa Mateyu; achita phwando ndi okhometsa msonkho; afunsidwa funso lokhudza kusala kudya |
||||||
Yudeya |
Alalikira m’masunagoge |
|||||
31, Pasika |
Yerusalemu |
Achiritsa mwamuna wina ku Betesida; Ayuda ayamba kufuna kumupha |
||||
Kubwerera kuchokera ku Yerusalemu (?) |
Ophunzira abudula ngala za tirigu pa Sabata; Yesu ndi “Mbuye wa Sabata” |
|||||
Galileya; Nyanja ya Galileya |
Achiritsa dzanja pa Sabata; khamu la anthu liyamba kumutsatira; achiritsa anthu enanso ambiri |
|||||
Phiri la pafupi ndi Kaperenao |
Anthu 12 asankhidwa |
|||||
Pafupi ndi Kaperenao |
Ulaliki wa paphiri |
|||||
Kaperenao |
Achiritsa wantchito wa kapitawo |
|||||
Naini |
Aukitsa mwana wa mkazi wamasiye |
|||||
Tiberiyo; Galileya (Naini kapena pafupi) |
Yohane ali m’ndende atumiza ophunzira ake kwa Yesu; Yesu atamanda Yohane |
|||||
Galileya (Naini kapena pafupi) |
Mzimayi wochimwa athira mafuta pamapazi ake; fanizo la angongole |
|||||
Galileya |
Ulendo wachiwiri wolalikira m’Galileya ndi atumwi 12 |
|||||
Waziwanda achiritsidwa; tchimo losakhululukidwa |
||||||
Alembi ndi Afarisi afuna kuona chizindikiro |
||||||
Mayi ake a Yesu ndi mchimwene wake abwera; anena kuti achibale ake ndi ophunzira ake |