4-E
Zochitika Zikuluzikulu M’moyo wa Yesu Padziko Lapansi—Utumiki Waukulu wa Yesu M’Galileya (Gawo 3) ndi ku Yudeya
NTHAWI |
MALO |
CHOCHITIKA |
MATEYU |
MALIKO |
LUKA |
YOHANE |
---|---|---|---|---|---|---|
32, pambuyo pa Pasika |
Nyanja ya Galileya; Betsaida |
Akukwera ngalawa n’kupita ku Betsaida, achenjeza za chofufumitsa cha Afarisi; achiritsa wosaona |
||||
Kaisareya wa Filipi |
Makiyi a Ufumu; aneneratu za imfa yake ndi kuukitsidwa |
|||||
Mwina pa phiri la Herimoni |
Akusandulika; Mawu a Yehova akumveka |
|||||
Kaisareya wa Filipi |
Achiritsa mnyamata wogwidwa ndi ziwanda |
|||||
Galileya |
Aneneratunso za imfa yake |
|||||
Kaperenao |
Ndalama yokakhomera msonkho iperekedwa mozizwitsa |
|||||
Wamkulu kwambiri mu Ufumu; anena fanizo la nkhosa yosochera ndi la kapolo wosakhululuka |
||||||
Galileya, Samariya |
Pa ulendo wopita ku Yerusalemu, auza ophunzira kuika patsogolo za Ufumu |
Utumiki wa Yesu Wakumapeto ku Yudeya
NTHAWI |
MALO |
CHOCHITIKA |
MATEYU |
MALIKO |
LUKA |
YOHANE |
---|---|---|---|---|---|---|
32, Chikondwerero cha Misasa |
Yerusalemu |
Aphunzitsa anthu pa Chikondwerero cha Misasa; asilikali atumidwa kuti amange Yesu |
||||
Anena kuti “Ine ndine kuwala kwa dziko”; achiritsa munthu wobadwa osaona |
||||||
Mwina ku Yudeya |
Atumwi 70 atumizidwa kukalalikira; abwerako akusangalala |
|||||
Yudeya; Betaniya |
Afotokoza za Msamariya wachifundo; apita kunyumba kwa Mariya ndi Marita |
|||||
Mwina ku Yudeya |
Aphunzitsanso pemphero lachitsanzo; anena fanizo lokhudza kulimbikira kupemphera |
|||||
Achotsa ziwanda pogwiritsa ntchito chala cha Mulungu; akananso kusonyeza Alembi ndi Afarisi chizindikiro |
||||||
Adya ndi Mfarisi; adzudzula chinyengo cha Afarisi |
||||||
Fanizo la wachuma wopanda nzeru ndi la Mtumiki woyang’anira nyumba wokhulupirika |
||||||
Achiritsa mkazi wolumala pa Sabata; fanizo la kanjere ka mpiru ndi la zofufumitsa |
||||||
32, Chikondwerero cha Kupereka Kachisi kwa Mulungu |
Yerusalemu |
Fanizo la M’busa wabwino; Ayuda ayesa kumuponya miyala; anyamuka n’kupita ku Betaniya wa kutsidya la Yorodano |