Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

16-B

Wiki Yomaliza ya Moyo wa Yesu Padziko Lapansi (Gawo 2)

Wiki Yomaliza ya Moyo wa Yesu Padziko Lapansi (Gawo 2)

Nisani 12

MADZULO (Masiku Achiyuda amayamba ndi kutha dzuwa litalowa)

M’MAWA

  • Yesu ali ndi ophunzira ake

  • Yudasi akonza zom’pereka

MADZULO

Nisani 13

MADZULO

M’MAWA

  • Petulo ndi Yohane akonzekera Pasika

  • Yesu ndi atumwi ena afika madzulo

MADZULO

Nisani 14

MADZULO

  • Adya Pasika ndi atumwi ake

  • Asambitsa mapazi a atumwi ake

  • Auza Yudasi kuti achoke

  • Ayambitsa mwambo wa Chakudya Chamadzulo cha Ambuye

  • Aperekedwa ndi kumangidwa m’munda wa Getsemane

  • Atumwi athawa

  • Aimbidwa mlandu ndi Khoti Lalikulu la Ayuda kunyumba kwa Kayafa

  • Petulo akana Yesu

M’MAWA

  • Aonekeranso m’Khoti Lalikulu la Ayuda

  • Apita naye kwa Pilato, kenako kwa Herode, n’kubwereranso kwa Pilato

  • Aweruzidwa kuti aphedwe ndipo aphedwera ku Gologota

  • Afa cha m’ma 3 koloko madzulo

  • Achotsa mtembo wake n’kukauika m’manda

MADZULO

Nisani 15 (Sabata)

MADZULO

M’MAWA

  • Pilato avomereza zoika alonda pamanda a Yesu

MADZULO

Nisani 16

MADZULO

  • Agula zonunkhira zina zopaka mtembo wa Yesu

M’MAWA

  • Aukitsidwa

  • Aonekera kwa ophunzira ake

MADZULO