Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

16-A

Wiki Yomaliza ya Moyo wa Yesu Padziko Lapansi (Gawo 1)

Wiki Yomaliza ya Moyo wa Yesu Padziko Lapansi (Gawo 1)

Nisani 8 (Sabata)

MADZULO (Masiku Achiyuda amayamba ndi kutha dzuwa litalowa)

  • Afika ku Betaniya masiku 6 Pasika asanachitike

M’MAWA

MADZULO

Nisani 9

MADZULO

  • Achita phwando panyumba ya Simoni wakhate

  • Mariya adzoza Yesu mafuta a nado

  • Ayuda afika kudzaona Yesu ndi Lazaro

M’MAWA

  • Khristu alowa mu Yerusalemu monga wopambana

  • Aphunzitsa pakachisi

MADZULO

Nisani 10

MADZULO

  • Akhala usiku wonse ku Betaniya

M’MAWA

  • Alawirira kupita ku Yerusalemu

  • Athamangitsa amalonda ogulitsa pa kachisi

  • Yehova alankhula kuchoka kumwamba

MADZULO

Nisani 11

MADZULO

M’MAWA

  • Akuphunzitsa mu kachisi, pogwiritsa ntchito mafanizo

  • Adzudzula mwamphamvu Afarisi

  • Kakhobidi ka mkazi wamasiye

  • Pa Phiri la Maolivi, aneneratu za kugwa kwa Yerusalemu ndi kunena za chimene chidzakhale chizindikiro cha kukhalapo kwake

MADZULO