Ziwerengero Zonse za 2023
Maofesi a Nthambi a Mboni za Yehova: 85
Mayiko Amene Anatumiza Lipoti: 239
Mipingo Yonse: 118,177
Opezeka pa Chikumbutso Padziko Lonse: 20,461,767
Amene Anadya Zizindikiro Padziko Lonse: 22,312
Ofalitsa Onse Amene Anagwira Ntchito Yolalikira a: 8,816,562
Avereji ya Ofalitsa Amene Ankalalikira Mwezi Uliwonse: 8,625,042
Kuwonjezereka kwa Ofalitsa Kuchokera mu 2022: 1.3
Obatizidwa Onse b: 269,517
Avereji ya Apainiya c Okhazikika Mwezi Uliwonse: 1,570,906
Avereji ya Apainiya Othandiza Mwezi Uliwonse: 738,457
Maola Onse Amene Tinalalikira: 1,791,490,713
Avereji ya Maphunziro a Baibulo d Mwezi Uliwonse: 7,281,212
Chaka cha utumiki cha 2023 chinayambira pa 1 September 2022, ndipo chinatha pa 31 August 2023.
a Wofalitsa ndi munthu amene amalalikira mwakhama uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu. (Mateyu 24:14) Kuti mudziwe mmene timapezera chiwerengerochi, onani nkhani ya pa jw.org yakuti “Kodi a Mboni za Yehova Alipo Angati Padziko Lonse?”
b Kuti mudziwe zimene mungachite kuti mubatizidwe n’kukhala wa Mboni za Yehova, onani nkhani ya pa jw.org yakuti “Kodi Ndingatani Kuti Ndikhale wa Mboni za Yehova?”
c Mpainiya ndi wa Mboni wobatizidwa komanso wachitsanzo chabwino amene amadzipereka kuti azilalikira uthenga wabwino kwa maola enaake mwezi uliwonse.
d Kuti mudziwe zambiri, onani nkhani ya pa jw.org yakuti “Kodi Phunziro la Baibulo Lomwe a Mboni za Yehova Amachititsa Limakhala Lotani?”