Mfundo Zanga—Makolo Anu
Chigawo 6
Mfundo Zanga—Makolo Anu
Lembani vuto limene limakusowetsani mtendere kwambiri panyumba panu komanso chifukwa chake mumavutika kwambiri kuthana nalo.
․․․․․
Malinga ndi zimene mwawerenga m’chigawo chino, kodi mukuganiza kuti mungathetse bwanji vuto limene mwalemba pamwambapa?
․․․․․