Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Lowani mu Mpumulo wa Mulungu

Lowani mu Mpumulo wa Mulungu

AHEBERI 4:11

M’mawa

  • 9:40 Kumvetsera Nyimbo

  • 9:50 Nyimbo Na. 87 ndi Pemphero

  • 10:00 Kodi Tingalowe Bwanji mu Mpumulo wa Mulungu?

  • 10:15 Kodi “Mawu a Mulungu Ndi Amoyo”—Mu Njira Yotani?

  • 10:30 Pitirizani Kudalira Yehova Kuti Azikutsogolerani

  • 10:55 Nyimbo Na. 89 ndi Zilengezo

  • 11:05 Yehova Amadalitsa Anthu Omvera

  • 11:35 Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa

  • 12:05 Nyimbo Na. 32

Masana

  • 1:20 Kumvetsera Nyimbo

  • 1:30 Nyimbo Na. 49

  • 1:35 Zochitika pa Moyo Wachikhristu

  • 1:45 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda

  • 2:15 Nkhani Yosiyirana: Amasangalatsa Mtima wa Yehova

    • • Achinyamata

    • • Alongo

    • • Achikulire

  • 3:00 Nyimbo Na. 38 ndi Zilengezo

  • 3:10 Muzitumikira Yehova Mosangalala

  • 3:55 Nyimbo Na. 118 ndi Pemphero