Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mupeze Mayankho a Mafunso Awa

Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
  1. 1. Kodi tingalowe bwanji mu mpumulo wa Mulungu? (Gen. 2:​1-3; Aheb. 4:​1, 11)

  2. 2. Kodi tingatani kuti mphamvu ya “mawu a Mulungu” isinthe moyo wathu? (1 Ates. 2:13; Aheb. 4:12)

  3. 3. N’chifukwa chiyani tiyenera kudalira Yehova kuti azititsogolera? (Yes. 26:​7-9, 15, 20)

  4. 4. Kodi tiyenera kuchita zotani kuti Yehova atidalitse? (1 Pet. 1:​13-15; 1 Yoh. 5:3)

  5. 5. Kodi tingatani kuti tizisangalatsa mtima wa Yehova? (Sal. 71:​14, 15; Aroma 12:2; 1 Pet. 4:10)

  6. 6. Mungatani kuti muzisangalala potumikira Yehova? (Yoh. 5:17)

© 2023 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

CA-brpgm24-CN