Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
1. Kodi timasonyeza bwanji kuti ‘tikuyembekezera Yehova’ mofunitsitsa? (Sal. 130:5, 6)
2. Kodi tingatani kuti tiziyembekezera Yehova mofunitsitsa pa nthawi zovuta? (Hab. 2:3, 4; 2 Tim. 4:2; Luka 2:36-38)
3. Kodi tingagwiritse ntchito bwanji mwanzeru nthawi yathu pamene tikuyembekezera tsiku la Yehova? (2 Pet. 3:11-13)
4. N’chifukwa chiyani tiyenera kumayembekezera Yehova tikamakumana ndi mavuto? (Sal. 62:1, 2, 8, 10; 68:6; 130:2-4)
5. Kodi tiyenera kuchita chiyani kuti tidzalandire mphoto ya olungama? (Sal. 58:11)
© 2023 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
CA-copgm24-CN