Ntchito Yolalikira ndi Kuphunzitsa Padziko Lonse
PADZIKO LONSE
-
MAYIKO 240
-
OFALITSA 8,340,847
-
NTHAWI IMENE TINATHERA POGWIRA NTCHITO YOLALIKIRA 1,983,763,754
-
MAPHUNZIRO A BAIBULO 10,115,264
M'CHIGAWO ICHI
Africa
Werengani zimene a Mboni ena anakumana nazo komanso zimene a Mboni za Yehova achita pa ntchito yophunzitsa Baibulo ku Ghana, Guinea-Bissau, Liberia, Malawi, Togo komanso Sierra Leone.
America
Zimene a Mboni ena anakumana nazo ku Brazil, Haiti, Mexico, United States ndi Venezuela.
Asia ndi Middle East
Zimene zinachitika ku Hong Kong, Mongolia, Philippines ndi Sri Lanka.
Europe
Werengani zimene zinachitikira a Mboni ena a ku Azerbaijan, Britain, Bulgaria, Georgia, Denmark, Hungary, Norway ndi Ukraine.
Oceania
Nkhani zochititsa chidwi zochokera ku Australia, Guam, New Caledonia, Papua New Guinea ndi Timor-Leste.