Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

GAWO 5 • MACHITIDWE 15:1-35

“Atumwi ndi Akulu Anasonkhana”

“Atumwi ndi Akulu Anasonkhana”

MACHITIDWE 15:6

Mumpingo munayambika nkhani yovuta imene ikanasokoneza mtendere komanso mgwirizano wa Akhristu. Kodi malangizo othetsera nkhani imeneyi anachokera kuti? M’gawoli, tiona mmene mpingo wa m’nthawi ya atumwi unkayendera, ndipo anthu a Mulungu masiku ano amatsanzira chitsanzo chimenechi.