Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

GAWO 3 • MACHITIDWE 10:1–12:25

‘Anthu a Mitundu Ina Analandira Mawu a Mulungu’

‘Anthu a Mitundu Ina Analandira Mawu a Mulungu’

MACHITIDWE 11:1

Kodi otsatira Yesu a Chiyuda akanavomereza kukalalikira uthenga wabwino kwa anthu a mitundu ina omwe anali osadulidwa? M’gawoli, tiona mmene mzimu wa Yehova unathandizira Akhristu kuti azikonda anthu a mitundu ina ndi kupewa tsankho. Tionanso mmene kuchita zimenezi kunawathandizira kuti ayambe kugwira mwakhama ntchito yochitira umboni kwa anthu a mitundu yonse.